Kutengela Dela lakwathu omwe akumapanga kabaza ndi anthu ochuluka kwambiri Choncho pa tsiku zimatheka kusuka njinga zokwana 15 kapena kuposela apo Ndimagwilisa ntchito ma backet(bigili)yomwe ili njila yochedwa kwambiri kuti ndimalize njinga zonsezo Zimanditengela nthawi yochulaka kwambiri kuti ndimalize chifukwa chosowa machine osukila(pressure washer) Njinga imodz ndimasuka pa mtengo wa K3000 Pa 3000 ya njinga...