Ndinaphunzira kupanga ma briquettes makala amene timapanga kuchokera ku zotsalira zokolora zakuminda monga mapetsi ndimakoko ngati amzimbe kapena zinyalala ndiye timapanga kukhala makala ndikumagulitsa,makala awa ndi abwino chifukwa timapanga pompanda kudula mitengo zimene zimene zikuthandidza kubwedzeletsa chilengedwe dziko muno. Ngakhale ndimapedza zinyalala mongotola koma sindikwanitsa kupanga makala ambiri...