Business yoweta nkhuku ndi ndiwo, komanso madzira muli protein ndekuti anthu ondizungulira health yawo izasintha akazayamba kudya nkhuku zimenezi,zitosi za nkhuku ndi manyowa tizizathira mmunda komanso tizaika ka garden kamasamba pakhomo pompo momwe tizagwirisa ntchito manyowawo kuti masamba azizabiliwira bwino mwathanzi ndipo masambawo azizakhalanso kutithandiza kundiwo za pakhomopo ndi maneba anthu tizakhala...