Bussines ya ma jumbo ndi yabwino chifukwa aliyese upita kutsika kukagula ndiwo amagula jumbo Kooda jumbo yoti uzigulitsa k200 umakaoda k64,000 amankhal ma pc 500 ndiye kuti K200500=100,000 Profit ndi k36,000 Nditha kupindulA kwambiri tamagula katundu wambiri