Busnes yake ndyoti ndiziipangira pa msika pomwe ndimapanga kale komanso ndimayenda mmamidzi kukagula ma scrap ama4n okufa komaso kumagulitsaso ma phone a new1 a keypad ndi buznes yoti kuyamba ndi 300000 potha pamiyezi iwiri ndingathe kubweretsa 900000 chifukwa ma scrap amaphone per kg ndi 500 to 600 southand mk choncho sindimaikaikira buznez iyi chifukwa mmamidzi timayendamoso timakhala ndanyamata oti...