Ok ineyo mutandipatsa mwayi oti nditsekule LIQUOR SHOP ndithakupanga phindu coz this business simashota ma customer chifukwa anthu ambir amaona kuti malo abwino achezerapo ndipamene palichakumwa komanso amaona kt akamwa mowa amakhara ndichisangalaro nde naneso naganizako kuti nditapeza mwayi ngat umenewuwu ndingakhare osangalala kwambir coz ndimasophenya anga kudzakwanilitsa zinthu ngat zimenezi or mutawonaso nokha...