Kwaineo nditakhala kuti ndapeza 3mita ndalama imenei nditha kuigawa magulu atatu agrodealer, barbershop ndi agent choyamba nditha kupeza malo oti ndizigulirapo mbeu kenako nditha kugula scale, lonner yoti ndizizaikapo matumba ndi masaka chachiwili nditha kutenga kutenga k200, 000 ndugula zipangizo za barbershop monga machine ometera, grass, extension, ma chart ndi mipando chachitatu nditha kupangitsa ma card a agent...