I will be doing my business i.e kabaza WA njinga ya at kawalazi tea estate .why kawalazi estate 1. Ma galimoto amavuta ( akapita mamawa ku mzuzu amabwerako mazuro which means akakuthawa ndekut ulendo umenewo wajomba which means trusted mode of transport ndi njinga za moto . 2. , people prefer motorcycle than cars. This is so because magalimoto amanyamka mamawa kwambiri 5:30 going mzuzu zomwe zimapangisa kuti anthu...