ZIKWAMA ZA BELLO SHOP ndi bizinesi yogulitsa zikwama za quality monga za sukulu, za laptop, ndi zaulendo koma za mu belo. Pakadali pano ndimagulitsa koma mozikoloweka mkumayenda nazo m'midzi kuno ku area 44,lilongwe koma kufunikira kulipo kwakukulu kotsekula shop. Ndi k3,000,000 nditsegula shop yoyamba ya zikwama ku Area 44 kuti ndithandize anthu opitilira 5,000 omwe pakadali pano amapita ku Town kukagula zikwama...