I want to startup a poultry farming yomwe yingathandize chigawo chakwathu ( jenda). Ndinadzayensapo koma ndimomwe zinthu zinariri yinagwa kamba ka (lockdown ) koma nditapedza thandizo ngati iri I'm very sure nditha kumagulitsa ndithu
Agriculture - Startup / Early Operations - Top entries