Bussines ndi ngapane ndi yogulisa mphunga nyemba mafuta omphikila ufa mazila ufa wa soya komaso tedza kukhala ndi chigayo chongayisa sinjilo and pop corn komaso fulawa Bussines yimeneyi ndiyomwe moyomwana ndi mayiona kuti yingasithe moyo wanga nditakhala kupanga yimeneyi