Ndikapeza mpata woti ndapeza Mpamba woyambira business iyi, ungandithandize mzambiri chifukwa ungandibweretsere chakudya pa nyumba komaso ungandithandize kuti ndiziyimire pa ndekha komaso kunthandiza azibale anga muzambiri chifukwa ena ali Ku school ndikhoza kuwalipirira school fees. Business yomwe ndanenayi ndiyabwino kwambiri chifukwa anthu ambiri akupindula nayo ndikuona anthu ambiri apindula ndi business...