Zomwe ndingapange ndi 3 million imeneyi ndtha kuwoda Zinthu zomwe anthu amazifuna kwambiri pamoyo watsiku nditsiku monga; Mazira ,Mafuta ophikira ,Mchere, shuga, soya Pieces mitundu yose ,Mafuta odzola ,thumba lakhobwe ,nyemba, mpunga,Kamba ,Jigis, sweets for kids,chigubu cha Mafuta ophikila ,Sopo ochapila both powders and Tablets including sopo osambira osayiwalaso ma painkillers. Zinthu zina ndtha kuoda matochi...