Kaunjika buznez kuphatikiza nd sapato za bello mostly magwarad abello kumapanga order ku lilongwe ndkumakagulitsa kumisika yakutal monga chiingeni ,kampepuza ,Pengapenga,manjiwira,ntonda Golomoti & kansinje. Withing a month capital ikhoza kumafika 10 mita