Ine business imene ndikuhaniza ndi yomaodetsa sugar koma so kugulisa ngat pa retail kutengela ndikuona kwathu kuno pa MCHinji boma ndi anthu ochepa amene amagulisa sugar basi nditapatsidwa mwai wa ndalama imenei ndikhoza kuyamba shop yogulisa sugar only chifukwa sugar business ndi yofunika kwambiri kutengela kuti pa ma family ten amene tikaonetsetsa samagwiritsa ntchito sugar akhoza kukhala mwina ndi family imodzi...