My business it's all about poultry,3 million itha kundithandiza muzambili ndisanayambe zonsezo pa 3 million ndichosapo 100 thousand yachikhumi kukasiya ku church inayo kuyambapo za ulimi wanga waziweto. Mwana piye pano ndi 2500 ndi ndikatenga anapiye ankhuku zachizungu 150 ndie kuti ndi MK 375000 ndie kuti ndigulaso matumba amakala awili 50,000 zodyera za nkhuku ndikhomesa 4 ma 10,000 imene ili 40,000.mbaula zanga...