Kaunjika ndi business yogulitsa zovala ndi nsapato za second hand. Ndimagula zovala ndi nsapato pa mtengo wotsika, kenako ndimazigulitsa kwa anthu pamtengo wokwanira. Cholinga changa ndi kupereka zovala zabwino, zaukhondo komanso zokongola zomwe anthu angakwanitse kugula. Business imeneyi ikundithandiza kupeza ndalama komanso kuthandiza anthu kupeza zovala zabwino pamtengo wotsika. Ndikufuna kukulitsa business yanga...