Ndufuna nzikaoda zinthu kuchokera ku South Africa zovala komanso ma cosmetics. Katunduyu mzamufuna shop mu city center chifukwa ndimafuna kuzizabwera anthu ambilimbili kuchokera madera osiyasiyana Malondawa azazdiwika chifukwa ndizizanenerera mma social media kudzera pa tsamba langa ka mchezo komanso kudzatsegula tsamba lokhudza malonda angawo komanso masamba ena otchukawa