Ndikufuna kuyamba business yogulitsa mbatatesi kumakaoda ku bembeki kumakaodesa ku wakawaka or ku 6 Miles Imawina kwambiri thumba la ndowa zitatu akugulitsa pa mtengo wa 40 thousand pamene kugulitsa nditha kumagulitsa 80 thousand,kugula matumba 10 imene ili 400 thousand ikhoza kumawina 300 thosand 1000 ya transport munthu sungakhale chimodzi modzi p0