Ulimi ndimaona ngati ndi njira yokhayo yomwe ingamupangitse munthu aliyense kupita chitsogolo ndi maso mphenya ake. Choncho ine ndikuona kuti nditakhala kuti ndili ndi engine kapena kuti pampu ya madzi yomwe ndikhoza kumagwiritsa ntchito pochitira ulimi wa thilira. CHIFUKWA CHIYANI NDIMAKHUMBIRA ULIMI WA THILIRA KUKHALA GWERO LOKWANIRITSIRA MASO MPHENYA ANGA? Choyamba...kwathu komwe ine ndimakhala ndi MBALI mwa...