MY BUSINESS IDEA: YOUTH PIG FARMING PROJECT Ndikufuna kuyambitsa Youth Pig Farming Project, business yomwe idzayang'ane pa kuweta nkhumba kuti ndizigulitsa kwa anthu komanso ogulitsa nyama. Ndinasankha business imeneyi chifukwa nyama ya nkhumba ili ndi msika, ndipo ndikufuna kupanga business yomwe ingandithandize kukhala wodzidalira komanso kupanga mwayi wa ntchito kwa achinyamata ena. Ngati ndapatsidwa MK3,000,000...