Business yanga ndiwabwino ndithu ndimapanga barbershop km chifukwa chisowa zipangizo ma kasitomala amatithawa amapita kukametetsa kutali kamba kotsata kukongola kwapamalo ndi zipangizo zamwe ife ndikuchepekedwa kwathu sitingakwanitse mwachitsazo ndimatha kumumeta munthu pa 2pin munthuyoso kumandiwuza kt apa ndy wandimeta bwino km bwanji osagula zithu zofunika kumeta komweku town timapeleka 10pin ndy nditati ndili...