Okondedwa sir /madam Ndimachokela lilongwe area 24 ndilindimaganizo oyamba business koma kuthekela ndilibe chifukwa mapezedwe anga sikotheka kuti ndingayambetu business ndichifukwa ndakufikila inu polemba kalatayitu Maganizo anga ndi otsegula shop yogulitsa zinthu izi mpunga,nyemba,soya ,tedza ,nkhobwe .ndizina zambiri business iyi ku ku banja kwanthu apangako ndikuziwa mavuto amakunanawo ndipo ndinaphunzila...