Ndimaoda ndikuguritsa anyezi,ku msika wa Bypass ku area 38 ndimaguritsa anyezi ma size osiyanasiyana wamkulumukulu kwambiri, okulirapo wapakatikati komanso Wang'onong'ono.Ndimapezeka ndi anyezi wamuwisi(fresh) komanso woumisa(dry) milingo yosiyanasiyana ndimayeza ma bigiri 5litres ,10litres komanso mu net ya 25kg,komanso ndimayeza pa sikero muringo ulionse umene kasitomara wafuna ndimamuyezela,chimodzimozinso...