CHIKONDI EYEWEAR/SUNGLASSES SHOP ndi business yogulitsa ma glass adzuwa(sunglasses) komaso ma glass amaso kwa amene Ali ndi vuto la maso(reading glasses). Ndili ndi ukadaulo pa business iyi komaso ndili ndi makasitomala ambiri chifukwa ndinayiyamba chaka Cha 2022. Ndilibe shop ndipo ndimangoyenda yenda maboma ngati Salima,nkhotakota ndi mangochi ndipo khumbo langa ndilotsekura shop Madera amenewa. Ndi ndalama...