Ndufuna ndizioda ndiwo zosiyanasiyana kuchokera Madera osiyanasiyana. nkumakagulitsa ma Dera osiyanasiyana komanso maiko otizungulira monga Zimbabwe, Zambia, Mozambique, Tanzania etc. Ndikufuna ndizakhazikitse ma likulu anga Madera angapo kuti nsombazi zisamasowe komanso zizipezeka mosavuta, malo ambiri. Ndufuna anthu azizatha kungoimba phone kuti tiwapititsore msomba pakhomo pawo.