Ndikupanga business yoti itha kuthandiza aliyense dziko la Malawi, pakusoka ma pantie achikadzi komaso achimuna omwe nditha kumagulisa zigawo zonse za dziko muno. Komaso athu atha kukhala ndi mwayi oti azizaoda nkumagulisa mmadela momwe akukhala. Pasegula sikuli yomwe nditha kumawaphunzisa athu luso kuti nawo azathe kuyamba zawo komaso kusegula ma company awo oti atha kumapanga zawo. Kulemba athu ntchito.