Kusonkhanisa magalimoto owonongeka ndkuwabwezeresa mu new model then ndkumawagulisa pAmitengo yokwera kusiyanisa ndimene unaodera magalimoto aja ndicholinga chofuna kupeza kapamwamba posatengera mitengo yowoderayo kenako nditha kusiyanisa Kaye ndi anthu amene akukadzitengera okha kunja pAmitengo yawo Yao zitakhara kut zilibwino ndtha kupezerapo anyamata ena ot zitha kundithandizira pena ndipena ndicholinga CHOTI...