Ngati ndili. ndi MK3 million business yomwe ndingapang ndi Mwachitsanzo: 1. MK1,000,000 — bizinesi yomwe imayenda pafupipafupi (monga grocery, ma snacks, kapena malonda ena). 2. MK1,000,000 — kuyisunga ngati ndalama yosungira/emergency. MK500,000 — kuphunzira luso la ntchito zamanja,kapena kugula zida zomwe zingakuthandizeni kupanga ndalama. MK500,000 — mugwiritse ntchito pang'onopang'ono malinga ndi mwayi...