Timapanga katundu monga ma cake,ma buns,samoosa ngat za bakery. Timapanganso peanut butter komanso jam ndi tomato source.Cholinga cha business imenei ndikufuna itazafika pa restaurant ndikukhala okhazikika pa malonda ndikupeleka katundu wa bwino kwa ma customers athu komanso kupelekela katundu ma shop oziwika bwino malawi monga Sana, shop wise ndi ena ambiri komaso kukhala ndi njira za makono zothandizila ma...