Am staying in karonga chilumba and kuweta nkhuku zomwe zilizachikuda ndi business chifukwa umakagulisa pakamodzi kuno kukaronga kumabwera ma tanzanian amene amagula nkhuku or utakhala nazo five hundred pakamodzi I already have a nkhola lomwe ndimawetelamo koma the challenge am facing ndi feed basi komasi ndufuna incubator yomwe ndizigwilisa ntchito kuswesa madzila nkhuku zikayamba kuswa madzila. Business imenei...