Ndimafuna ntamagulitsa mpunga wanga pa chitipa Boma,kumakaoda k karonga chifukwa kunoko mpunga wambiri kulibe,people go to karonga and sell here so I want people ordering rice from me.Ndithaso wina kumagulitsa k isongole chifukwa Amati mpunga wa Malawi umakoma compare Nd kwaoko(Tanzania)nditha kumapeza phindu lochuluka nditati ndigulitsa business chifukwa nditha kukhala big supplier.