Choyamba ndipeza Malo abwino owetera nkhuku ndikugula tikhuku tating'ono zokwana 1,000,000 ndikuzimangila mpanda wa bwino zomwe ziononge ndalama zokwana 1,500,000 . Kenako ndalama yosalayo ndikagula makhwala a k200,000 zomwe zindithandizire pa matenda kenako ndikugula zakunya za k500,000 inayo ndikumasovera timavuto tomwe ndizikumana nawo