Yanjinga yamoto yakabaza ndiyabwino kwambli ngat njingayo ndiyako chifukwa chot dairy umakhala kut ukupanga ndalama. Ineo mot ndilipano ndipangapo bezinesi imeneo kma ndinkaona kut zimatheka chifukwa chot tsiku ililonse ndinkakwanitsa kumupatsa mwino njingayo ndalama yokwana 10,000 tsiku lililonse .