Business yanga ili ndi miyezi itatu chiyambireni mu miyezi imeneyi ndaona kuti business ndichithu chofunika pamoyo wamuthu chifukwa ndikumatha kusiyanitsa ndi ndalama yomwe ndimapeza ndikamapanga timaganyu. Ngakhale business yake ili ndi katundu ocheperapo koma ndikumakwanitsa kudya ndikuchotsaso yalendi pompo komaso kuiwodera ndikagulitsa takatunduti . Ngakhale zili chomwechi mavuto samalera zimakhoza kutheka tsiku...