Business idea yanga ndiyozatsegula shop yomwe tizapange lent ndikumagulitsa ndikuwodetsa zovala .koma tizizalora achinyamata omwe tawapeza kuti ndiwokhulupilika kuti azizatha kutenga zovala ndikukagulitsa olo alibe mpamba owodera ndikumazapeleka ndlama yowodera zkatheka pakatha nthawi yomwe tagwilizana. Izi zizathandiza anthu omwe akusowa zochita kupeza mwayi ochita business ndikupeza zosowa pa miyoyo yawo.business...