Ndizagula njinga yamoto 850k yomwe izizapanga ndalama zosachepera 10k patsiku,1mita ndizailowetsa ku ulimi wa nkhuku za white, ubwino wake makola alipo komaso knowledge about nkhuku za white ndilinayo yokwanira bwino,500k idzakwana kundipezetsa anapiye osachepera 200 ndyekuti 500k ndiyokwana kugula zokudya komaso zipangizo zomwe zingazaperewere advantage Ina izakhala kuti mkati mwa ndime njinga ija ikupangaso...