???? NKHUKU SHARE BUSINESS – MWAYI WOPANGA PHINDU Business yanga ndi njira yothandizira anthu kupeza nkhuku ndi kuyamba ulimi wa nkhuku popanda ndalama zambiri. Timapereka nkhuku kwa munthu kuti azisamalira ndi kubereketsa. Ikabereka, timagawana ana ake mogwirizana ndi malamulo a business. Mwachitsanzo, munthu akalandira nkhuku imodzi, ikabereka timagawana ana ake. Munthuyo amabweza nkhuku yomwe tinamupatsa...