Business yanga ndiyolima ndikugulitsa chimanga Cha popcorn mwachindunji Kwa makampani ndi amalonda akuluakulu M'malawi muno. Ndondomeko yanga ndiyoyika chidwi ndi Khama m'munda kudzera mukugwiritsa ntchito mbewu yapamwamba ya popcorn hybrid pamodzi ndi kasamalidwe kofunika pakukulitsa zokolola zambiri. Munda wanga ndizayendetsa mwa kuthira ndowe za ziweto m'nthaka, kuthira feteleza wofunika wa m'masitolo komaso...