Brain's engineering welding companys ndi business ya welding yomwe idzakhare kasungu yomwe idzidzapereka ntchito zapamwamba zaget , still door, still windows , thank stand cholinga kuthana ndivuto lomwe customer amakumanalo kuchedwa kwantchito welders chifukwa chosowa zipangizo zapamwamba zogwilila ntchito komaso kusowa kwachitsimikizo Ndindalama za 3 million ndiyamba business yaphavu kwambili ndizida zodalilika ngt...