Business yanga ndi ya kaunjika wama jeans ???? yemwe ndimagulitsira mu mntown ya Lilongwe mu street ya Bwaila.business iyi imayenda koma osati kwambiri chifukwa cha supply ndiyochulka kwambiri mu mntown yathu ya Lilongwe. Timapitabe daily kukathamanga pofuna kufikira Pena pake popeza sikadza kokha ndiposo kufuna kupewa zambiri .koma siziyenda kweni kweni malingana ndi momwe ndanenera kuti supply ndiyochuluka ndiposo...