Kuweta khuku zachikuda plus kugulisa tima phone tama keypads also ma airpods . 400pin kumangila khola loti nkhuku zizikhalama 1500 kugula zodyela khuku like momwela madzi ndi ma deya 650 kusaka khuku anapiye zoti zowetazo after miyezi kumagulisa anthu ozungulila Dela mwanthu kapena ena angazikonde amadela ozungulila then kupeza malo oti xilimamo ma samba manyowa ochekela Ku khuku zithilamo then kumaoda tima phone...