Ndimapanga ma bed, table ndi Zina zambiri, ndnaphunzila za carpentry kuzela mwa bamboo anga omwe nda carpenter even my grandfather was a carpenter. Kuchita mwayi kukhala nd capital yochuluka choncho zingathandize kwambiri kukhazikika. komaso ndapeza ganyu ndkazungulila ndizizakhazikika pa malo. Ndmapangaso za mobile money koma chifukwa choti capital ndiochepa ndmapangila pa khomo ngat kungula ma bundles ndi zina...