Kutsagula Shop ya Kugula ndi kugulitsa Mbewu Za ulimi komaso Mafuta Ophikira, Mbewu zomwe Zizidzapezeka ndi : Chimanga, soya, Mpunga, Nyemba, Mtedza, Nandolo, khobwe, popcorn ndi Mbewu zina Zomwe ma Customer a Mderali amafuna. Zolinga zanga pa bussines ndikuthandiza athu kupeza Mbewu Mosavuta komaso pa Mitengo ya bwino , Mtsogolo kuyamba kugula Mbewu zambir pa thawi yokolola kuti zizigulitsidwa mtengo ukakwera(...