Kuyamba ulimi woweta Nkhunda pa mlingo wokulira . zimenezi kuti zitheke pakufunika mbewu yabwino ya Nkhunda,makola aakulu bwino komanso otetezeka ku zinthu monga matenda,akuba,komanso zinyama zomwe zingaononge ziweto za Nkhunda.ndasankha Nkhunda pa zifukwa zotsatirazi;Malo,Nkhunda sikhoza kuwetedwa zambiri pa Malo ochepa.chifukwa china ndi choti ,Nkhunda zimapilira kumatenda mosiyana ndi ziweto Zina za mgulu la...