Panopa ndimatenga ma olders a anthu then akatumiza half of the money ndimamutumizira nyamata waku Tanzania yemwe amaodetsa online ndi kutumiza kuno ku Malawi it take three days kut katundu afike mu Lilongwe then akafika ma customer amamaliza kulipira ndalama Ine nkuwapatsa katundu wawo