Car wash ndi business yabho kwambili km imaoneka yonyozeka chifukwa anthu ambili amaziyang'ana kaye iwowo km ndi business yamPhavu kusuka magalimoto ndikwa simple zimangofunika kukhara munthu oziwa zipangizo komaso kagwilidwe ka ntchito yo ndi 3mita ndi business yotheka kugura ma chine awili ma brush ma spray kenako kupeza malo oti uzipangirapo business km malo amafunika Akhara musika kpn mpepete mwa nsewu kpn...