Ndilibe business iliyose koma ndikufunitsitsa nditamapanga ulimi wankhumba. Mu ulimi umenewu muri phindu lochuluka limene ndingapeze komaso kuthandzira moyo watsiku nditsiku ndi K3Milion imeyi nditha kugura nkhunba zazikaz 5ndzazimuna 5 mjuyamba kuweta imene ir pafupifupi 750000 inayo nditha kumangira makola ndikgura zakudya komaso kusunga ina ya katemera. Mu ulimi wankhunba umenwu nditha kuyambaso ulimi wanthilira...