Masomphenya anga ndiofuna kuchita Ulimi wakasakaniza . Choncho ndikuganiza zoyamba kuweta nkhumba ndi mbuzi nkumachitanso ulimi wambeu ngat mpunga nthawi ya dzinja ndi chimanga ntawi ya chilimwe ,ndikubyalanso mitengo ya chamwamba (Moringa trees) Ndikufuna kuyamba ndi nkhumba 4 ndi mbuzi 8 , kwinaku half ekala ya mpunga . Nyengo ya mvula ikatha kuyamba nthirila nkumabyala chimanga chozagulitsa dowe poti ntawiyi...