ndimaweta nkhuku za nyama zomwe ukazisamalira bwino umapeza phindu lochuluka ndimatenga ma 150 to 200 day old chicks ,ndimazigulisa zikakwana 6 weaks,,150 chicks ndimagula pa mtengo wa 3000 each, zimadya 12 bags 50kg per bag pa mtengo wa 139 each bag